Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  February 2016

February 15-21

NEHEMIYA 9-11

February 15-21
 • Nyimbo Na. 84 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Anthu Okhulupirika Amatsatira Malangizo a Gulu la Yehova”: (10 min.)

  • Neh. 10:28-30—Anamvera zoti asakwatirane ndi “anthu a m’mayikowo” (w98 10/15 21 ndime 11)

  • Neh. 10:32-39—Iwo anatsimikiza kuti azithandiza pa kulambira koona (w98 10/15 21 ndime 11-12)

  • Neh. 11:1, 2—Anamvera ndi mtima wonse malangizo a gulu la Yehova (w06 2/1 11 ndime 6; w98 10/15 22 ndime 13)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Neh. 9:19-21—Kodi Yehova anasonyeza bwanji kuti amapereka kwa anthu ake zinthu zofunika? (w13 9/15 9 ndime 9-10)

  • Neh. 9:6-38—Kodi Alevi anapereka chitsanzo chotani pa nkhani yopemphera? (w13 10/15 22-23 ndime 6-7)

  • Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: Neh. 11:15-36 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 19

 • Moyo Wabwino Kwambiri”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuonetsa vidiyo. Kenako kambiranani mafunso. Funsani wofalitsa mmodzi yemwe ali pabanja kapena amene sali pabanja yemwe wachita zambiri potumikira Yehova asanalowe m’banja. (1 Akor. 7:35) Kodi anadalitsidwa bwanji?

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 26 ndime 1-9 (30 min.)

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 76 ndi Pemphero