ONANI

455 B.C.E.

 1. Nisan (Mar./Apr.)

  2:4-6 Nehemiya anapempha chilolezo chomanganso Yerusalemu yemwe anali likulu la kulambira koona panthawiyo

 2. Iyara

 3. Sivani

 4. Tamuzi (June/July)

  2:11-15 Nehemiya anafika ku Yerusalemu panthawi imeneyi ndipo anayendera mpanda wa mzindawo

 5. Aba (July/Aug.)

  3:1; 4:7-9 Anayamba kumanga ngakhale kuti ankatsutsidwa

 6. Eluli (Aug./Sept.)

  6:15 Anamanga mpandawo masiku 52

 7. Tishiri