Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Alongo a ku Indonesia akulalikira pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mverani Mulungu

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU February 2016

Zitsanzo za Ulaliki

Zitsanzo za ulaliki wa Galamukani! ndi Mverani Mulungu. Gwiritsani ntchito zitsanzozi kuti mupange ulaliki wanu umene mungagwiritse ntchito.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Nehemiya Ankakonda Kulambira Yehova

Yerekezani kuti mukuona zimene Nehemiya anachita poyesetsa kuti amangenso mpanda n’kuthandiza anthu kuti azilambiranso Yehova. (Nehemiya 1-4)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Nehemiya Anali Woyang’anira Wabwino

Anathandiza Aisiraeli kuti azilambira Mulungu mosangalala. Yerekezani kuti mukuona zimene zinachitika ku Yerusalemu mwezi wa Tishri mu 455 B.C.E. (Nehemiya 8:1-18)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anthu Okhulupirika Amatsatira Malangizo a Gulu la Yehova

Masiku a Nehemiya anthu anayambanso kulambira Yehova ndipo anachita zinthu zosiyanasiyana. (Nehemiya 9-11)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Moyo Wabwino Kwambiri

Achinyamata akhoza kuchita zambiri m’gulu la Yehova. Gwiritsani ntchito mafunso awa pokambirana vidiyo.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Tikuphunzira kwa Nehemiya

Yerekezani kuti mukuona Nehemiya akuteteza mwakhama kulambira koona (Nehemiya 12-13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Itanirani Anthu Onse M’gawo Lanu ku Chikumbutso!

Chitsanzo cha ulaliki pogawira kapepala koitanira ku Chikumbutso cha 2016. Ngati munthu wasonyeza chidwi chitani zomwe tasonyeza

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Esitere Anapulumutsa Anthu a Mulungu

Yerekezani kuti mukumuona Esitere akuteteza anthu a Mulungu molimba mtima. (Esitere 1-5)