CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Munthu Amene Ankazunza Akhristu Anakhala Mkhristu Wakhama”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Mac. 9:4​—N’chifukwa chiyani Yesu anafunsa Saulo kuti: “N’chifukwa chiyani ukundizunza?” (bt 60-61 ¶5-6)

  • Mac. 10:6​—N’chifukwa chiyani n’zochititsa chidwi kuti mtumwi Petulo ankakhala kunyumba kwa munthu wofufuta zikopa? (Simoni, wofufuta zikopa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mac. 10:6, nwtsty)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mac. 9:10-22

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 58

 • Zofunika Pampingo: (8 min.)

 • Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 16

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero