8:20-23

Amuna 10 ochokera m’zilankhulo zonse za anthu a mitundu ina, adzagwira chovala cha munthu amene ndi Myuda ndi kunena kuti: “Anthu inu tipita nanu limodzi.” M’masiku otsiriza ano, anthu a mitundu yonse akubwera kudzalambira Yehova limodzi ndi Akhristu odzozedwa

Kodi a nkhosa zina amathandiza Akhristu odzozedwa m’njira ziti masiku ano?

  • Amagwira nawo ntchito yolalikira ndi mtima wonse

  • Amathandiza ntchito yolalikira ndi ndalama zawo