• Nyimbo Na. 49 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Musachoke ‘M’chigwa cha Pakati pa Mapiri’”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Zek. 12:3​—Kodi Yehova anasandutsa bwanji Yerusalemu kukhala “mwala wotopetsa”? (w07 12/15 22-23 ¶9-10)

  • Zek. 12:7​—N’chifukwa chiyani Yehova adzayambirire kupulumutsa “mahema a Yuda”? (w07 12/15 25 ¶13)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Zek. 12:1-14

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.6 14-15Muitanireni kumisonkhano yathu.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.6​tsamba 14 ndi 15. Sonyezani mmene mungapangire ulendo wobwereza pogwiritsa ntchito magazini imene munamusiyira pa ulendo woyamba. Kenako muitanireni kumisonkhano yathu.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) jl phunziro 5​—Muitanireni kumisonkhano yathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 98

 • Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.

 • Mbali Yatsopano pa Misonkhano ya Mkati mwa Mlungu”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo ya Betefage, Phiri la Maolivi ndi Yerusalemu.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 11 ¶22-28 komanso tsamba 117

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 5 ndi Pemphero