Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  December 2016

December 26–January 1

YESAYA 17-23

December 26–January 1
 • Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Munthu Akamagwiritsa Ntchito Udindo Wake Molakwika Amachotsedwa pa Udindowo”: (10 min.)

  • Yes. 22:15, 16—Sebina anagwiritsa ntchito udindo wake mongofuna kudzipindulitsa yekha (ip-1 238-239 ¶16-17)

  • Yes. 22:17-22—Yehova anachotsa Sebina pa udindo n’kuikapo Eliyakimu (ip-1 238-240 ¶17-18)

  • Yes. 22:23-25—Tingaphunzire zambiri pa zimene zinachitikira Sebina (w07 1/15 9 ¶1; ip-1 240-241 ¶19-20)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yes. 21:1—Kodi ndi dera liti lomwe ankalitchula kuti “chipululu cha nyanja,” ndipo n’chifukwa chiyani? (w06 12/1 11 ¶2)

  • Yes. 23:17, 18—Kodi phindu ndi malipiro a mzinda wa Turo zinakhala bwanji zinthu “zopatulika kwa Yehova”? (ip-1 253-254 ¶22-24)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 17:1-14

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) bhsGwiritsani ntchito vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo kuti mugawire bukuli. (Dziwani izi: Musaonetse vidiyoyi m’chitsanzochi.)

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) bhsYambitsani phunziro la Baibulo lachidule ndipo muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 151 ¶10-11Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 44

 • Kodi ‘Mudzakhalabe Maso’?: (8 min.) Nkhani yokambidwa ndi mkulu yochokera mu Nsanja ya Olonda ya March 15, 2015, tsamba 12-16. Limbikitsani onse kuti apitirize kukhala maso mofanana ndi mlonda amene Yesaya anatchula komanso anamwali 5 ochenjera a m’fanizo la Yesu.—Yes. 21:8; Mat. 25:1-13.

 • Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo yakuti, Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 14 ¶1-13.

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero