Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

December 19-25

YESAYA 11-16

December 19-25

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Dziko Lapansi Lidzadzaza ndi Anthu Odziwa Yehova”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yes. 11:1, 10—Kodi Yesu Khristu angakhale bwanji nthambi yotuluka “pachitsa cha Jese” ndiponso “muzu wa Jese”? (w06 12/1 9 ¶6)

  • Yes. 13:17—N’chifukwa chiyani Baibulo limanena kuti Amedi ankaona kuti siliva si kanthu komanso sankasangalala ndi golide? (w06 12/1 10 ¶10)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 13:17-22; 14:1-8

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yobu 34:10—Kuphunzitsa Choonadi.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Mlal. 8:9; 1 Yoh. 5:19—Kuphunzitsa Choonadi.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 54 ¶9—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU