Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO DECEMBER 2016

December 12-18

YESAYA 6-10

December 12-18
 • Nyimbo Na. 116 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Mesiya Anakwaniritsa Ulosi”: (10 min.)

  • Yes. 9:1, 2—Malemba ananeneratu kuti adzagwira ntchito yolalikira ku Galileya (w11 8/15 10 ¶13; ip-1 124-126 ¶13-17)

  • Yes. 9:6—Adzakhala ndi maudindo ambiri (w14 2/15 12 ¶18; w07 5/15 6)

  • Yes. 9:7—Ulamuliro wake udzabweretsa mtendere weniweni ndiponso chilungamo (ip-1 132 ¶28-29)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yes. 7:3, 4—N’chifukwa chiyani Yehova anapulumutsa Ahazi yemwe anali mfumu yoipa? (w06 12/1 9 ¶4)

  • Yes. 8:1-4—Kodi ulosi umenewu unakwaniritsidwa bwanji? (it-1-E 1219; ip-1 112 ¶23-24)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 •   Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 7:1-17

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g16.6 chikuto

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g16.6 chikuto

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 34 ¶18—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU