Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 TIMOTEYO 1-4

“Mulungu Sanatipatse Mzimu Wamantha”

“Mulungu Sanatipatse Mzimu Wamantha”

1:7, 8

Mawu ouziridwa amene mtumwi Paulo analembera Timoteyo angatipatse mphamvu kuti tizichita zinthu molimba mtima. Sitiyenera kumachita manyazi ndi uthenga wabwino. M’malomwake tiyenera kumalalikira molimba mtima ngakhale zitakhala kuti tikhoza “kumva zowawa.”

Kodi ndiyenera kusonyeza kulimba mtima pa nthawi ziti?