Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

August 26–September 1

AHEBERI 4-6

August 26–September 1
 • Nyimbo Na. 5 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yesetsani Kuti Mulowe Mumpumulo wa Mulungu”: (10 min.)

  • Aheb. 4:1, 4​—Kodi tsiku la mpumulo wa Mulungu n’chiyani? (w11 7/15 24-25 ¶3-5)

  • Aheb. 4:6​—Muzimvera Yehova (w11 7/15 25 ¶6)

  • Aheb. 4:9-11​—Musamangoyendera maganizo anu (w11 7/15 28 ¶16-17)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Aheb. 4:12​—Kodi “mawu a Mulungu” amene akutchulidwa palembali ndi ati? (w16.09 13)

  • Aheb. 6:17, 18​—Kodi “zinthu ziwiri zosasinthika” zimene zatchulidwa palembali ndi ziti? (it-1 1139 ¶2)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aheb. 5:1-14 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU