Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 1-3

Muzikonda Chilungamo Ndipo Muzidana ndi Kusamvera Malamulo

Muzikonda Chilungamo Ndipo Muzidana ndi Kusamvera Malamulo

1:9

Yesu amakonda chilungamo ndipo amadana ndi chilichonse chomwe chinganyozetse dzina la Atate ake.

Kodi tingatengere bwanji chitsanzo cha Yesu pa nkhani yokonda chilungamo

  • tikamayesedwa kuti tichite chiwerewere?

  • wachibale wathu akachotsedwa?