Akugwira ntchito pa Beteli ku Wallkill, New York

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU August 2019

Zimene Tinganene

Zitsanzo za ulaliki zofotokoza zinthu zomwe Mulungu walonjeza kudzachita m’tsogolo.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Mulungu Sanatipatse Mzimu Wamantha”

Tikamadalira Mulungu kuti atithandize, tikhoza kumachita zinthu molimba mtima tikamakumana ndi mayesero.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzicheza ndi Anthu Amene Amakonda Yehova

Anthu amene timacheza nawo angachititse kuti tikhale ndi makhalidwe abwino kapena oipa

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Uike Akulu”

Abale amene amatsogolera mumpingo wachikhristu amasankhidwa mogwirizana ndi zimene Malemba amanena.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Achinyamata, Mukhale “Odzipereka pa Ntchito Zabwino”

Kodi wachinyamata angakwaniritse bwanji cholinga chawo chokhala mpainiya wothandiza kapena wokhazikika?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzikonda Chilungamo Ndipo Muzidana ndi Kusamvera Malamulo

Kodi mungasonyeze bwanji kuti mumakonda chilungamo komanso kuti mumadana ndi kusamvera malamulo?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yesetsani Kuti Mulowe Mumpumulo wa Mulungu

Kodi tingalowe bwanji mumpumulo wa Mulungu, nanga tingatani kuti tisachokemo?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Ntchito Zabwino Zimene Yehova Sangaziiwale

Kodi muyenera kukwaniritsa zinthu ziti kuti mukatumikire pa Beteli?