CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Chipulumutso Chanu Chikuyandikira”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Luka 21:33​—Kodi mawu a Yesu palembali akutanthauza chiyani? (“Kumwamba ndi dziko lapansi zidzachoka” “mawu anga sadzachoka ayi” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 21:33, nwtsty)

  • Luka 22:28-30​—Kodi ndi pangano liti limene Yesu anakhazikitsa ndipo anapangana ndi ndani, nanga lidzakwaniritsa chiyani? (w14 10/15 16-17 ¶15-16)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 22:35-53

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene. Kenako sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri.

 • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene. Kenako sonyezani zimene mungachite ngati mwininyumba ali wotanganidwa.

 • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU