CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Zomwe Tikuphunzira M’fanizo la Ndalama 10 za Mina”: (10 min.)

  • Luka 19:12, 13​—“Munthu wina wa m’banja lachifumu” asanachoke, anapatsa akapolo ake ndalama kuti achite bizinesi mpaka adzabwere (jy 232 ¶2-4)

  • Luka 19:16-19​—Akapolo okhulupirika anali ndi luso losiyanasiyana koma aliyense analandira mphoto (jy 232 ¶7)

  • Luka 19:20-24​—Zinthu sizinamuyendere bwino kapolo woipa yemwe sanachite malonda ndi ndalama imene anapatsidwa (jy 233 ¶1)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Luka 19:43​—Kodi mawu a Yesuwa anakwaniritsidwa bwanji? (adzamanga mpanda wazisonga kukuzungulira” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 19:43, nwtsty)

  • Luka 20:38​—Kodi zimene Yesu ananenazi zikutitsimikizira bwanji kuti akufa adzaukitsidwa? (“pakuti kwa iye onsewa ndi amoyo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 20:38, nwtsty)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 19:11-27

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU