N’CHIFUKWA CHIYANI KULIMBA MTIMA N’KOFUNIKA?

KODI TINGASONYEZE BWANJI KULIMBA MTIMA?

  • Tiziganizira zimene Yehova anachita populumutsa anthu.​—Eks. 14:13

  • Tizipemphera kuti Mulungu atithandize kukhala olimba mtima.​—Mac. 4:29, 31

  • Tizidalira Yehova.​—Sal. 118:6

Kodi ndiyenera kulimbana ndi zinthu ziti zimene zimandichititsa mantha ndikamatumikira Mulungu?

ONERANI VIDIYO YAKUTI MUZIPEWA ZINTHU ZIMENE ZINGAWONONGE KHALIDWE LANU LA KUKHULUPIRIKA—KUOPA ANTHU, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • N’chifukwa chiyani kulimba mtima n’kofunika tikakhala mu utumiki?

  • Kodi lemba la Miyambo 29:25 likusonyeza bwanji kusiyana pakati pa kuopa anthu ndi kukhulupirira Yehova?

  • Kodi n’chifukwa chiyani tiyenera kukhala olimba mtima panopa?