CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Udindo Waukulu wa Mlonda”: (10 min.)

  • Ezek. 33:7​—Yehova anaika Ezekieli kukhala mlonda (it-2 1172 ¶2)

  • Ezek. 33:8, 9​—Mlonda akachenjeza anthu ankapewa mlandu wamagazi (w88 1/1 28 ¶13)

  • Ezek. 33:11, 14-16​—Yehova adzapulumutsa anthu amene amamvera akachenjezedwa (w12 3/15 15 ¶3)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Ezek. 33:32, 33​—N’chifukwa chiyani tiyenera kupitirizabe kulalikira ngakhale kuti anthu ena amatitsutsa kapena kutinyoza? (w91 3/15 17 ¶16-17)

  • Ezek. 34:23​—Kodi vesi limeneli likukwaniritsidwa bwanji? (w07 4/1 26 ¶3)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 32:1-16

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.4 chikuto​—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.4 chikuto​—Muitanireni kumisonkhano.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 2 ¶9-10​—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU