Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  August 2017

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 28-31

Yehova Anapereka Cholowa kwa Anthu Omwe Sankamulambira

Yehova Anapereka Cholowa kwa Anthu Omwe Sankamulambira

29:18-20

Ngati Yehova anapereka mphoto kwa anthu omwe sankamulambira chifukwa cha ntchito imene anagwira, ndiye kuli bwanji kwa atumiki ake okhulupirika?

ZIMENE ABABULO ANACHITA

Anagonjetsa mzinda wa Turo

ZIMENE INEYO NDIKUCHITA

Kodi ndikuchita zotani pankhondo yanga yauzimu?

MMENE ABABULO ANADZIPEREKERA

  • Anazinga mzinda wa Turo kwa zaka 13

  • Asilikali a Babulo ankasowa zinthu zina pamoyo wawo

  • Ababulo sanapatsidwe malipiro aliwonse

MMENE NDIKUDZIPEREKERA

Kodi ndimachita zotani potumikira Yehova?

KODI YEHOVA ANAWAPATSA CHIYANI ABABULO?

Yehova anawapatsa dziko la Iguputo kuti alande chuma chake

MADALITSO AMENE YEHOVA WANDIPATSA

Kodi Yehova wandipatsa madalitso otani?