40:10, 14, 16

  • Zipinda za alonda komanso zipilala zimatithandiza kudziwa kuti Yehova ali ndi mfundo zapamwamba za makhalidwe abwino zokhudza kulambira koyera

  • Dzifunseni kuti, ‘Kodi ndingasonyeze m’njira ziti kuti ndimatsatira mfundo zapamwamba komanso zolungama za Yehova?’