Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  August 2017

August 28–September 3

EZEKIELI 39-41

August 28–September 3
 • Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Mmene Masomphenya a Ezekieli Onena za Kachisi Akutikhudzira”: (10 min.)

  • Ezek. 40:2​—Kulambira Yehova n’kokwezeka kwambiri kuposa kulambira kwa mtundu wina uliwonse (w99 3/1 11 ¶16)

  • Ezek. 40:3, 5​—Yehova adzakwaniritsa cholinga chake chokhudza kulambira koyera (w07 8/1 10 ¶2)

  • Ezek. 40:10, 14, 16​—Tiyenera kutsatira mfundo zapamwamba za makhalidwe abwino za Yehova kuti tizimulambira m’njira yovomerezeka (w07 8/1 11 ¶5)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Ezek. 39:7​—N’chifukwa chiyani tinganene kuti anthu akamaimba mlandu Mulungu kuti ndi amene amachititsa zinthu zopanda chilungamo, amakhala akudetsa dzina lake? (w12 9/1 21 ¶2)

  • Ezek. 39:9​—Pambuyo pa nkhondo ya Aramagedo, kodi zida zankhondo zimene mitundu idzasiye zidzagwiritsidwa ntchito yotani? (w89 8/15 14 ¶20)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 40:32-47

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) fg phunziro 1 ¶1​—Yambani ndi kumufotokozera za vidiyo yakuti Kodi Mungakonde Kumva Uthenga Wabwino? (koma musaonetse vidiyoyi). Kenako perekani kabukuko.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) fg phunziro1 ¶2—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 1 ¶3-4

MOYO WATHU WACHIKHRISTU