Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  August 2017

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 35-38

Gogi wa ku Magogi Awonongedwa Posachedwapa

Gogi wa ku Magogi Awonongedwa Posachedwapa

Baibulo limafotokoza zimene zidzachitike Gogi wa ku Magogi asanawonongedwe komanso akadzawonongedwa.

 • Chiv. 17:16-18

  Kodi chisautso chachikulu chidzayamba ndi kuwonongedwa kwa chiyani?

 • Ezek. 38:2, 11, 15

  Kodi anthu a Yehova adzaukiridwa ndi ndani?

 • Chiv. 16:16

  Kodi Yehova adzawononga Gogi wa ku Magogi pankhondo iti?

 • Chiv. 20:4

  Kodi Khristu adzalamulira kwa zaka zingati?

Kodi ndingatani kuti ndidzakhale wokonzeka pamene Gogi wa ku Magogi adzaukire anthu a Mulungu?