92:12

Mtengo wa kanjedza umatha kukhala zaka zoposa 100 koma n’kumaberekabe zipatso. Nawonso achikulire akhoza kumachitabe zambiri mofanana ndi mtengo umenewu

Achikulire akhoza kumachita zotsatirazi:

92:13-15

  • Kupempherera ena

  • Kuphunzira Baibulo

  • Kusonkhana komanso kupereka ndemanga

  • Kuuza ena zomwe zinawachikira pa moyo wawo

  • Kulalikira ndi mtima wonse