Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  August 2016

August 8-14

MASALIMO 92-101

August 8-14
 • Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Mukhoza Kumachitabe Zambiri Ngakhale Muli Okalamba”: (10 min.)

  • Sal. 92:12—Olungama amabereka zipatso (w07 9/15 32; w06 7/15 13 ndime 2)

  • Sal. 92:13, 14—Okalamba akhoza kumachitabe zambiri ngakhale mphamvu zawo zili zochepa (w14 1/15 26 ndime 17; w04 5/15 12 ndime 9-10)

  • Sal. 92:15—Okalamba akhoza kulimbikitsa ena powafotokozera zomwe akumana nazo pa moyo wawo (w04 5/15 12-14 ndime 13-18)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Sal. 99:6, 7—N’chifukwa chiyani tinganene kuti Mose, Aroni komanso Samueli ndi zitsanzo zabwino? (w15 7/15 8 ndime 5)

  • Sal. 101:2—Kodi mawu akuti, “Ndidzayendayenda m’nyumba yanga ndi mtima wanga wosagawanika” akutanthauza chiyani? (w05 11/1 24 ndime 14)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 95:1–96:13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Tsamba loyamba la g16.4—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Tsamba loyamba la g16.4—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 161-162 ndime 18-19—Thandizani wophunzirayo kuti aone mmene angagwiritsire ntchito mfundo za m’ndimezi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 90

 • Achikulire—Ndinu Ofunika Kwambiri (Sal. 92:12-15): (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yamutu wakuti, Achikulire—Ndinu Ofunika Kwambiri. (Pitani pamene alemba kuti MAVIDIYO ENA > BAIBULO.) Kenako funsani abale ndi alongo kuti afotokoze zomwe tikuphunzirapo. Pemphani abale ndi alongo achikulire kuti azithandiza achinyamata kusankha zinthu mwanzeru komanso aziwafotokozera zomwe anakumana nazo pa moyo wawo. Limbikitsani achinyamata kuti azipempha achikulire kuti aziwathandiza maganizo akamasankha zinthu zofunika kwambiri.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 4 ndime 1-15, komanso bokosi patsamba 39.

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero