• Nyimbo Na. 61 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Kodi Yehova Ndidzamubwezera Chiyani?”: (10 min.)

  • Sal. 116:3, 4, 8—Yehova anathandiza wolemba Masalimo kuti asaphedwe (w87-E 3/15 24 ndime 5; w09 7/15 29 ndime 4 )

  • Sal. 116:12—Wolemba Masalimo anatsimikiza mtima kumuthokoza Yehova chifukwa cha zimene anamuchitira (w09 7/15 29 ndime 4-5; w98 12/1 24 ndime 3)

  • Sal. 116:13, 14, 17, 18—Wolemba Masalimoyu ankayesetsa kuchita zonse zimene Mulungu amafuna komanso kukwaniritsa zinthu zonse zimene anamulonjeza (w10 4/15 27, komanso bokosi)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Sal. 110:4—Kodi palembali mawu akuti ‘kulumbira’ akutanthauza chiyani? (w14 10/15 11 ndime 15-17; w06 9/1 14 ndime 1)

  • Sal. 116:15—Pokamba nkhani ya maliro, n’chifukwa chiyani vesili siliyenera kugwiritsidwa ntchito ponena za munthu amene wamwalirayo? (w12 5/15 22 ndime 2)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 110:1–111:10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) ll 16—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) ll 17—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 179-181 ndime 17-19—Muthandizeni wophunzirayo kuti aone mmene angagwiritsire ntchito mfundo za m’ndimezi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU