N’chifukwa chiyani Aisiraeli anaiwala mwamsanga zimene Yehova anawachitira?

106:7, 13, 14

  • Anasiya kuganizira za Yehova n’kuyamba kuganizira mavuto komanso zofuna zawo

Kodi tingatani kuti tizithokoza Yehova komanso kuti tisamaiwale zomwe watichitira?

106:1-5

  • Tiziganizira zinthu zonse zimene Yehova watichitira

  • Tiziganizira zimene Mulungu walonjeza kudzatichitira m’tsogolo

  • Tizithokoza Yehova tikaona kuti watichitira zomwe tinapempha