• Nyimbo Na. 2 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Muziyamikira Yehova”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Sal. 109:8—Kodi Mulungu anakonzeratu zoti Yudasi apereke Yesu kuti ulosi ukwaniritsidwe? (w00 12/15 24 ndime 20; it-1-E 857-858)

  • Sal. 109:31—Kodi Yehova amaima bwanji “kudzanja lamanja la munthu wosauka”? (w06 9/1 14 ndime 8)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 106:1-22

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) ll 6—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) ll 7—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 178-179 ndime 14-16—Muthandizeni wophunzirayo kuona mmene angagwiritsire ntchito mfundo za m’ndimezi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 94

 • Yehova Adzatisamalira (Sal. 107:9): (15 min.) Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuonetsa vidiyo yakuti, Yehova Adzatisamalira. (Pitani pamene alemba kuti MAVIDIYO ENA > BANJA.) Pemphani omvera kuti afotokoze zimene tikuphunzirapo.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 5 ndime 1-13.

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 149 ndi Pemphero