Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Akulalikira pogwiritsa ntchito intakomu ku Vienna, m’dziko la Austria

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU August 2016

Zitsanzo za Ulaliki

Zitsanzo za Ulaliki wa magazini a Galamukani! komanso kabuku kakuti, Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha. Gwiritsani ntchito zitsanzozi kuti mupange ulaliki wanuwanu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Pitirizani Kukhala M’malo Otetezeka a Wam’mwambamwamba

Kodi malo otetezeka a Yehova ndi chiyani ndipo timakhala bwanji otetezeka tikakhala m’malowa? (Salimo 91)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Tizithandiza Ophunzira Baibulo Athu Kuti Adzipereke Komanso Kubatizidwa

N’chifukwa chiyani n’kofunika kwambiri kuti munthu adzipereke komanso kubatizidwa? Kodi mungachite chiyani kuti muthandize munthu amene mukuphunzira naye Baibulo kudzipereka komanso kubatizidwa?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mukhoza Kumachitabe Zambiri Ngakhale Muli Okalamba

Chaputala 92 cha Masalimo chimasonyeza kuti okalamba akhoza kumachitabe zambiri ngakhale ali ndi mphamvu zochepa.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amakumbukira Kuti Ndife Fumbi

Mu Salimo 103, Davide anagwiritsa ntchito mawu oyerekezera pofotokoza za kukoma mtima kwa Yehova.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

‘Muziyamikira Yehova’

Salimo 106 limatilimbikitsa kuti tizikhala ndi mtima woyamikira Mulungu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

‘Kodi Yehova Ndidzamubwezera Chiyani?’

Kodi wolemba masalimo anachita zotani kuti asonyeze kuyamikira kwake Yehova? (Salimo 116)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Kuphunzitsa Choonadi

Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulaliki chatsopano kuti mufotokoze mfundo inayake ya m’Baibulo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Tidzagwira Ntchito Yapadera Yogawira Nsanja ya Olonda mu September

Tidzagawira Nsanja ya Olonda imene ikufotokoza mmene Mulungu amatithandizira tikamakumana ndi mavuto.