5:38-42

  • Tikamalira chifukwa cha imfa ya munthu amene timam’konda, sizisonyeza kuti sitikhulupirira zoti akufa adzauka (Gen. 23:2)

  • Kuganizira nkhani za m’Baibulo zokhudza anthu amene anaukitsidwa kungatithandize kuti tisamakayikire zoti akufa adzauka

Kodi inuyo mumafuna mutadzaonananso ndi ndani, akufa akamadzaukitsidwa?

Kodi mumamva bwanji mukamaganizira zodzakumananso ndi anthu amenewo?