CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yesu Ali ndi Mphamvu Zoukitsa Anthu Amene Anamwalira”: (10 min.)

  • Maliko 5:38​—Timalira munthu amene timam’konda akamwalira

  • Maliko 5:39-41​—Yesu ali ndi mphamvu zoukitsa anthu amene “akugona” mu imfa (sanamwalire ayi, koma akugona” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 5:39, nwtsty)

  • Maliko 5:42​—‘Tidzasangalala kwambiri’ anthu akamadzaukitsidwa m’tsogolo (jy 118 ¶6)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Maliko 5:19, 20​—N’chifukwa chiyani Yesu pa nthawiyi anapereka malangizo osiyana ndi omwe ankapereka nthawi zonse? (“ukawauzemfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 5:19, nwtsty)

  • Maliko 6:11​—Kodi mawu akuti “sansani fumbi kumapazi anu” amatanthauza chiyani? (“sansani fumbi kumapazi anu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 6:11, nwtsty)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 6:1-13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene. Musonyezeni webusaiti ya jw.org.

 • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse loti mugwiritse ntchito komanso funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 36 ¶23-24​—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU