2:5-12

Kodi tikuphunzirapo chiyani pa chozizwitsa chimenechi?

  • Timadwala chifukwa chakuti tinatengera uchimo

  • Yesu ali ndi mphamvu zokhululukira machimo komanso kuchiritsa odwala

  • Mu Ufumu wa Mulungu, Yesu adzathetsa uchimo komanso matenda

Kodi lemba la Maliko 2:5-12 lingandithandize bwanji kupirira ndikamadwala?