Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  April 2017

April 17-23

YEREMIYA 25-28

April 17-23

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Khalani Olimba Mtima Ngati Yeremiya”: (10 min.)

  • Yer. 26:2-6​—Yehova anatuma Yeremiya kuti alengeze uthenga wochenjeza anthu (w09 12/1 24 ¶6)

  • Yer. 26:8, 9, 12, 13​—Yeremiya sanaope anthu amene ankadana naye (jr 21 ¶13)

  • Yer. 26:16, 24​—Yehova anateteza mneneri wake wolimba mtimayu (w09 12/1 25 ¶1)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yer. 27:2, 3​—Kodi n’chifukwa chiyani amithenga ochokera m’mitundu yosiyanasiyana anabwera ku Yerusalemu, nanga n’chifukwa chiyani Yeremiya anawapangira magoli? (jr 27 ¶21)

  • Yer. 28:11​—Kodi Yeremiya anachita bwanji zinthu mwanzeru pamene Hananiya ankamutsutsa, ndipo tikuphunzira chiyani pa chitsanzo chakechi? (jr 187-188 ¶11-12)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 27:12-22

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) T-36​—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) T-36​—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 7 ¶4-5​—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU