Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  April 2017

April 3-9

YEREMIYA 17-21

April 3-9
 • Nyimbo Na. 69 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Muzilola Kuti Yehova Aziumba Maganizo ndi Makhalidwe Anu”: (10 min.)

  • Yer. 18:1-4​—Woumba amasankha zimene akufuna kuchita ndi dongo limene akugwiritsa ntchito (w99 4/1 22 ¶3)

  • Yer. 18:5-10​—Yehova ndiye woyenera kulamulira anthu (it-2 776 ¶4, w13 6/15 25 ¶3-4)

  • Yer. 18:11​—Muzivomera ndi mtima wonse kuti Yehova akuumbeni (w99 4/1 22 ¶4-5)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yer. 17:9​—Kodi munthu angasonyeze bwanji kuti mtima wake wayamba kumunyenga? (w01 10/15 25 ¶13)

  • Yer. 20:7​—Kodi Yehova anagwiritsa ntchito bwanji mphamvu zake kuti akope Yeremiya? (w07 3/15 9 ¶6)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 21:3-14

• KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Kukambirana “Zitsanzo za Ulaliki.” Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo. Limbikitsani ofalitsa kuti abwererenso kwa anthu amene anawagawira kapepala kakuti Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 118

 • Zofunika Pampingo: (5 min.) Mukhoza kukambirana mfundo zimene tikuphunzira mu Buku Lapachaka. (yb16 22)

 • Muziwalandira ndi Manja Awiri”: (10 min.) Yambani ndi kukambirana nkhaniyi kwa 3 minitsi. Kenako onetsani vidiyo yakuti Steve Gerdes: Sitidzaiwala Mmene Anatilandirira.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 21 ¶1-12.

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 5 ndi Pemphero