Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  April 2017

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 29-31

Yehova Ananeneratu za Pangano Latsopano

Yehova Ananeneratu za Pangano Latsopano
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

Yehova ananeneratu kuti pangano la Chilamulo lidzalowedwa m’malo ndi pangano latsopano lomwe lidzapindulitse anthu kwamuyaya.

PANGANO LA CHILAMULO

 

PANGANO LATSOPANO

Yehova ndi mtundu wa Isiraeli

PAKATI PA

Yehova ndi Isiraeli wauzimu

Mose

MKHALAPAKATI

Yesu Khristu

Nsembe zanyama

LOTHEKA NDI

Nsembe ya Yesu

Miyala

LOLEMBEDWA PA

Mitima ya anthu