Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

April 24-30

YEREMIYA 29-31

April 24-30

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yehova Ananeneratu za Pangano Latsopano”: (10 min.)

  • Yer. 31:31​—Pangano Latsopano linanenedweratu kudakali zaka zambiri (it-1 524 ¶3-4; w10 3/15 26 ¶12-13)

  • Yer. 31:32, 33​—Pangano latsopano ndi losiyana ndi pangano la Chilamulo (jr 173-174 ¶11-12)

  • Yer. 31:34​—Pangano latsopano limatheketsa kuti machimo onse akhululukidwe (jr 177 ¶18)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yer. 29:4, 7​—Kodi n’chifukwa chiyani Ayuda omwe anapita ku ukapolo analamulidwa kuti ‘azifunira mtendere’ Babulo, nanga ifeyo tingatsatire bwanji mfundo imeneyi? (w96 5/1 11 ¶5)

  • Yer. 29:10​—Kodi vesi limeneli likusonyeza bwanji kuti maulosi a m’Baibulo ndi olondola? (g 6/12 14 ¶1-2)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 31:31-40

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Mat. 6:10​—Kuphunzitsa Choonadi.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yes. 9:6, 7; Chiv. 16:14-16​—Kuphunzitsa Choonadi.

 • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w14 12/15 21​—Mutu: Kodi Yeremiya Ankatanthauza Chiyani Ponena Kuti Rakele Akulirira Ana Ake?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU