Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  April 2017

April 10-16

YEREMIYA 22-24

April 10-16
 • Nyimbo Na. 52 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Kodi Muli ndi ‘Mtima Wodziwa’ Yehova?”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yer. 22:30​—Kodi lamuloli likusonyeza kuti Yesu sanali woyenera kukhala pa mpando wachifumu wa Davide? (w07 3/15 10 ¶9)

  • Yer. 23:33​—Kodi “katundu wa Yehova” n’chiyani? (w07 3/15 11 ¶1)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer 23:25-36

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.2 tsamba loyamba​—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.2 tsamba loyamba​—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 5 ¶1-2​—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU