Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO APRIL 2016

April 4-10

YOBU 16-20

April 4-10
 • Nyimbo Na. 79 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Tizilimbikitsa Anzathu Powayankhula Mokoma Mtima”: (10 min.)

  • Yobu 16:4, 5—Munthu wopereka malangizo ayenera kuyankhula molimbikitsa kwa ena (w90 3/15 27 ndime 1-2)

  • Yobu 19:2—Yobu analira chifukwa cha mawu opweteka a Bilidadi (w06 3/15 15 ndime 5; w94 10/1 32)

  • Yobu 19:25—Chiyembekezo chakuti akufa adzauka chinathandiza Yobu pa nthawi yomwe anakumana ndi mayesero aakulu (w06 3/15 15 ndime 4; it-2-E 735 ndime 2-3)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yobu 19:20 [Mawu am’munsi]—Kodi Yobu ankatanthauza chiyani pamene ananena kuti, “Ndapulumuka ndi khungu la mano anga”? (w06 3/15 14 ndime 13; it-2-E 977 ndime 1)

  • Yobu 19:26—Popeza kuti munthu sangathe kuona Yehova, kodi Yobu ankatanthauza chiyani ponena kuti “ndidzaona Mulungu”? (w94 11/15 19 ndime 17)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: Yobu 19:1-23 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani mavidiyo a zitsanzo za ulaliki ndipo kenako kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’mavidiyowo. Limbikitsani ofalitsa kuti akonze ulaliki wawowawo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU