Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  April 2016

April 25–May 1

YOBU 33-37

April 25–May 1
 • Nyimbo Na. 50 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Mnzako Weniweni Amakupatsa Malangizo Othandiza”: (10 min.)

  • Yobu 33:1-5—Elihu ankalemekeza Yobu (w95 2/15 29 ndime 2-4)

  • Yobu 33:6, 7—Elihu anali wodzichepetsa komanso wokoma mtima (w95 2/15 29 ndime 2-4)

  • Yobu 33:24, 25—Elihu analimbikitsa Yobu ngakhale pamene ankamupatsa malangizo (w11 4/1 23 ndime 3; w09 4/15 4 ndime 8)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yobu 33:24, 25—Kodi “dipo” limene Elihu ananena linkatanthauza chiyani? (w11 4/1 23 ndime 3-5)

  • Yobu 34:36—Kodi Yobu anafunika kuyesedwa kufika pati, nanga ifeyo tikuphunzirapo chiyani? (w94 11/15 17 ndime 10)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: Yobu 33:1-25 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: Gawirani kapepala koitanira anthu kumsonkhano wachigawo wa 2016, pogwiritsa ntchito chitsanzo cha ulaliki chomwe chili patsamba 8. (Osapitirira 2 min.)

 • Ulendo Wobwereza: fg phunziro 12 ndime 4-5—Chitani chitsanzo chosonyeza mmene tingachitire ulendo wobwereza kwa munthu amene analandira kapepala koitanira anthu kumsonkhano wachigawo. Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira. (Osapitirira 4 min.)

 • Phunziro la Baibulo: jl mutu 11. Limbikitsani wophunzirayo kuti adzapite kumsonkhano wachigawo. (Osapitirira 6 min.)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 124

 • Zofunika Kukumbukira Pamsonkhano Wachigawo”: (8 min.) Nkhani. Onetsani vidiyo yakuti Zofunika Kukumbukira Pamsonkhano Wachigawo (Vidiyo imeneyi ikupezeka pa jw.org pambali yakuti Zofalitsa Nkhani pa akaunti ya mpingo wanu.) Limbikitsani onse kuti ayesetse kukonzekereratu n’cholinga choti adzapezekepo masiku onse atatu. Pomaliza fotokozani dongosolo lomwe mpingo wanu udzatsatire pogwira ntchito yoitanira anthu kumsonkhano.

 • Zofunika pampingo: (7 min.)

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 29 ndime 11-15 (30 min.)

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero