Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Abale ndi alongo pamsonkhano wa mayiko mu 2014, ku New Jersey, U.S.A.

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU April 2016

Zitsanzo za Ulaliki

Mfundo zothandiza pogawira Galamukani! ndi buku la Baibulo Limaphunzitsa Chiyani. Gwiritsani ntchito zitsanzozi kuti mukonze ulaliki wanuwanu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tizilimbikitsa Anzathu Powayankhula Mokoma Mtima

M’malo momulimbikitsa anzake atatu a Yobu ankangomuonjezera ululu mwa kumuuza mawu osalimbikitsa komanso kumuimba milandu yabodza. (Yobu 16-20)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Nkhani Zatsopano Zothandiza Poyamba Kukambirana ndi Anthu

Gwiritsani ntchito nkhani yatsopano yamutu wakuti “Kodi Baibulo Limanena Zotani?” poyamba kukambirana ndi anthu

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yobu Sanalole Kuti Maganizo Olakwika Amusokoneze

Onani kusiyana kwa mabodza a Satana ndi mmene Yehova amationera. (Job 21-27)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yobu Ndi Chitsanzo Chabwino pa Nkhani ya Kukhala ndi Mtima Wosagawanika

Yobu ankayesetsa kutsatira mfundo za Yehova za makhalidwe abwino ndipo anali wachilungamo. (Yobu 28-32)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mnzako Weniweni Amakuuza Malangizo Othandiza

Muzikonda ena ngati mmene Elihu ankakondera Yobu. (Yobu 33-37)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

Ntchito Yoitanira Anthu Kumsonkhano Wachigawo

Zinthu zofunika kukumbukira pogawira timapepala toitanira anthu kumsonkhano wachigawo wa Mboni za Yehova. Yesererani chitsanzo cha ulaliki.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Zofunika Kukumbukira Pamsonkhano Wachigawo

Ganizirani mmene mungasonyezere ena chikondi pamsonkhano.