Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

Baibulo la pa Intaneti

BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA

Yobu 25:1-6

25  Tsopano Bilidadi+ wa ku Shuwa anayankha kuti:   “Ulamuliro ndi wake ndipo iye ndi wochititsa mantha.+ Iye amakhazikitsa mtendere kumwamba.   Kodi asilikali ake angatheke kuwawerenga? Ndipo ndani amene kuwala kwake sikum’fika?   Choncho, kodi munthu angakhale bwanji wolungama pamaso pa Mulungu?+ Kapena kodi munthu wobadwa kwa mkazi angakhale bwanji woyera?+   Kulitu mwezi koma si wowala. Ndipo nyenyezi si zoyera m’maso mwake.   Nanga kuli bwanji munthu yemwe ndi mphutsi, Komanso mwana wa munthu yemwe ndi nyongolotsi?”+

Mawu a M'munsi