Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Baibulo la pa Intaneti | BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA

Salimo 134:1-3

Nyimbo Yokwerera Kumzinda. 134  Tamandani Yehova,+Inu nonse atumiki a Yehova,+Inu amene mumaimirira m’nyumba ya Yehova usiku.+   Pamene mukupemphera mutakweza manja anu, muzikhala oyera,+Ndipo tamandani Yehova.+   Yehova, amene ndiye Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi,+Akudalitseni ali ku Ziyoni.+

Mawu a M'munsi