Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Baibulo la pa Intaneti | BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA

Salimo 133:1-3

Nyimbo ya Davide Yokwerera Kumzinda. 133  Taonani! Ndi zabwino komanso zosangalatsa kwambiri Abale akakhala pamodzi mogwirizana!+   Zili ngati mafuta abwino amene athiridwa pamutu,+ Amene akutsikira kundevu, Ndevu za Aroni,+ Amenenso akuyenderera mpaka m’khosi la zovala zake.+   Zili ngati mame+ a ku Herimoni,+ Amene akutsikira pamapiri a ku Ziyoni.+ Pakuti Yehova analamula dalitso kukhala kumeneko,+ Walamulanso kuti kukhale moyo mpaka kalekale.+

Mawu a M'munsi