Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Baibulo la pa Intaneti | BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA

Salimo 131:1-3

Nyimbo ya Davide Yokwerera Kumzinda. 131  Inu Yehova, mtima wanga sunadzikweze,+Maso anga si onyada.+Sindinafune zinthu zapamwamba kwambiri,+Kapena zinthu zodabwitsa kwambiri.+   Ine ndadzitonthoza ndipo ndakhazika mtima wanga pansi.+Ndakhala ngati mwana amene wangosiya kumene kuyamwa, amene ali m’manja mwa mayi ake.+Ndakhala ngati mwana amene wangosiya kumene kuyamwa.+   Isiraeli ayembekezere Yehova,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+

Mawu a M'munsi