Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Baibulo la pa Intaneti | BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA

Salimo 117:1, 2

117  Tamandani Yehova, inu mitundu yonse ya anthu.+ Mulemekezeni, inu mafuko onse.+   Pakuti kukoma mtima kosatha kumene watisonyeza ndi kwakukulu.+ Ndipo choonadi+ cha Yehova chidzakhalapobe mpaka kalekale. Tamandani Ya, anthu inu!+

Mawu a M'munsi