Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Baibulo la pa Intaneti | BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA

Salimo 100:1-5

Nyimbo yoyamikira.+ 100  Fuulirani Yehova mosangalala inu nonse anthu a padziko lapansi chifukwa wapambana.+   Tumikirani Yehova mokondwera.+ Bwerani kwa iye mukufuula mosangalala.+   Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+ Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+ Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+   Lowani pazipata zake ndi mawu oyamikira,+ Lowani m’mabwalo ake ndi mawu otamanda.+ Muyamikeni, tamandani dzina lake.+   Pakuti Yehova ndi wabwino.+ Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapo mpaka kalekale,+ Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwomibadwo.+

Mawu a M'munsi