Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

1 Mbiri 1:1-54

1  Adamu,+Seti,+Enosi,+   Kenani,+Mahalalele,+Yaredi,+   Inoki,+Metusela,+Lameki,+  Nowa,+Semu,+ Hamu+ ndi Yafeti.+  Ana a Yafeti anali Gomeri, Magogi,+ Madai,+ Yavani,+ Tubala, Meseke,+ ndi Tirasi.+  Ana a Gomeri anali Asikenazi,+ Rifati,+ ndi Togarima.+  Ana a Yavani anali Elisaha,+ Tarisi,+ Kitimu,+ ndi Rodanimu.+  Ana a Hamu anali Kusi,+ Miziraimu,+ Puti,+ ndi Kanani.+  Ana a Kusi anali Seba,+ Havila, Sabita,+ Raama,+ ndi Sabiteka.+ Ana a Raama anali Sheba ndi Dedani.+ 10  Kusi anabereka Nimurodi+ amene anali woyamba kukhala wamphamvu padziko lapansi.+ 11  Miziraimu anabereka Ludimu,+ Anamimu, Lehabimu, Nafituhimu,+ 12  Patirusimu,+ ndi Kasiluhimu+ (Afilisiti+ anachokera mwa iyeyu), ndiponso Kafitorimu.+ 13  Kanani anabereka Sidoni+ mwana wake woyamba, kenako anabereka Heti.+ 14  Anaberekanso Ayebusi,+ Aamori,+ Agirigasi,+ 15  Ahivi,+ Aariki, Asini,+ 16  Aarivadi,+ Azemari,+ ndi Ahamati.+ 17  Ana a Semu+ anali Elamu,+ Ashuri,+ Aripakisadi,+ Ludi,+ Aramu,Uzi, Huli, Geteri, ndi Masi.+ 18  Aripakisadi anabereka Shela,+ ndipo Shela anabereka Ebere.+ 19  Ebere anabereka ana awiri. Wina dzina lake anali Pelegi,*+ chifukwa m’masiku ake, dziko lapansi linagawikana. M’bale wakeyo dzina lake anali Yokitani. 20  Yokitani anabereka Alamodadi, Selefi, Hazaramaveti, Yera,+ 21  Hadoramu, Uzali, Dikila,+ 22  Obali, Abimaele, Sheba,+ 23  Ofiri,+ Havila,+ ndi Yobabi.+ Onsewa anali ana a Yokitani. 24  Semu,+Aripakisadi,+Shela,+ 25  Ebere,+Pelegi,+Reu,+ 26  Serugi,+Nahori,+Tera,+ 27  Abulamu,+ kutanthauza Abulahamu.+ 28  Ana a Abulahamu anali Isaki+ ndi Isimaeli.+ 29  Awa ndiwo mabanja awo: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+ 30  Misima, Duma,+ Maasa, Hadadi,+ Tema, 31  Yeturi, Nafisi, ndi Kedema.+ Amenewa ndiwo anali ana a Isimaeli. 32  Ketura+ mdzakazi*+ wa Abulahamu anabereka Zimirani, Yokesani, Medani,+ Midiyani,+ Isibaki,+ ndi Shuwa.+ Ana a Yokesani anali Sheba ndi Dedani.+ 33  Ana a Midiyani anali Efa,+ Eferi, Hanoki, Abida, ndi Elida.+ Onsewa anali ana aamuna a Ketura. 34  Abulahamu anabereka Isaki.+ Ana a Isaki anali Esau+ ndi Isiraeli.+ 35  Ana a Esau anali Elifazi, Reueli,+ Yeusi, Yalamu, ndi Kora.+ 36  Ana a Elifazi anali Temani,+ Omari, Zefo, Gatamu, Kenazi,+ Timina,+ ndi Amaleki.+ 37  Ana a Reueli anali Nahati, Zera, Shama, ndi Miza.+ 38  Ana a Seiri+ anali Lotani, Sobala, Zibeoni, Ana,+ Disoni, Ezeri, ndi Disani.+ 39  Ana a Lotani anali Hori ndi Homamu. Mlongo wake wa Lotani anali Timina.+ 40  Ana a Sobala anali Alivani, Manahati, Ebala, Sefo, ndi Onamu.+ Ana a Zibeoni anali Aya ndi Ana.+ 41  Mwana* wa Ana anali Disoni.+ Ana a Disoni anali Hemadani, Esibani, Itirani, ndi Kerana.+ 42  Ana a Ezeri+ anali Bilihani, Zavani, ndi Ekani.+ Ana a Disani anali Uzi ndi Arani.+ 43  Tsopano awa ndiwo mafumu amene analamulira dziko la Edomu+ ana a Isiraeli asanayambe kulamulidwa ndi mfumu ina iliyonse:+ Bela mwana wa Beori. Dzina la mzinda wake linali Dinihaba.+ 44  Patapita nthawi, Bela anamwalira ndipo Yobabi mwana wa Zera+ wa ku Bozira,+ anayamba kulamulira m’malo mwake. 45  Patapita nthawi, Yobabi anamwalira ndipo Husamu+ wa kudziko la Atemani,+ anayamba kulamulira m’malo mwake. 46  Patapita nthawi, Husamu anamwalira ndipo Hadadi+ mwana wa Bedadi, amene anagonjetsa Amidiyani+ m’dziko la Mowabu, anayamba kulamulira m’malo mwake. Dzina la mzinda wake linali Aviti.+ 47  Patapita nthawi, Hadadi anamwalira ndipo Samila wa ku Masereka+ anayamba kulamulira m’malo mwake. 48  Patapita nthawi, Samila anamwalira ndipo Shauli wa ku Rehoboti+ mzinda wa m’mphepete mwa Mtsinje,* anayamba kulamulira m’malo mwake. 49  Patapita nthawi, Shauli anamwalira ndipo Baala-hanani mwana wa Akibori+ anayamba kulamulira m’malo mwake. 50  Patapita nthawi, Baala-hanani anamwalira ndipo Hadadi anayamba kulamulira m’malo mwake. Dzina la mzinda wake linali Pau, ndipo mkazi wake dzina lake linali Mehetabele mwana wa Matiredi mwana wamkazi wa Mezahabu.+ 51  Patapita nthawi, Hadadi anamwalira. Mafumu a Edomu anali mfumu Timina, mfumu Aliva, mfumu Yeteti,+ 52  mfumu Oholibama, mfumu Ela, mfumu Pinoni,+ 53  mfumu Kenazi, mfumu Temani, mfumu Mibezari,+ 54  mfumu Magidieli, ndi mfumu Iramu.+ Amenewa ndiwo anali mafumu+ a Edomu.

Mawu a M'munsi

Dzina lakuti “Pelegi” limatanthauza, “Kugawika” ndiponso “Mtsinje.”
Onani Matanthauzo a Mawu Ena.
Mawu ake enieni, “ana.”
Umenewu ndi mtsinje wa Firate.