Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 NYIMBO 77

Kuwala M’dziko Lamdima

Sankhani Zoti Mumvetsere
Kuwala M’dziko Lamdima
ONANI

(2 Akorinto 4:6)

 1. 1. M’dzikoli mulitu mdima,

  Anthu sakumvera.

  Koma taona kuwala,

  Ngati m’bandakucha.

  (KOLASI)

  Uthenga wa M’lungu,

  Wawala ngati dzuwa

  M’dziko lamdimali.

  Ukupatsa anthu

  Onse chiyembekezo

  Mdima watha.

 2. 2. Tidzutse omwe agona,

  Poti nthawi yatha.

  Ndipo tiwalimbikitse,

  Tiwapempherere.

  (KOLASI)

  Uthenga wa M’lungu,

  Wawala ngati dzuwa

  M’dziko lamdimali.

  Ukupatsa anthu

  Onse chiyembekezo

  Mdima watha.