Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 NYIMBO 67

“Lalikira Mawu”

Sankhani Zoti Mumvetsere
“Lalikira Mawu”
ONANI

(2 Timoteyo 4:2)

 1. 1. Mulungu watilamula;

  Ndipo tikufunika kumvera.

  Tifotokozeretu anthu

  Adziwe chiyembekezo chathu.

  (KOLASI)

  Lalikira

  Indetu onse amve!

  Lalika,

  Dzikoli lisanathe.

  Lalika,

  Ofatsa amvetsetse.

  Lalika

  M’dziko lonse!

 2. 2. Mavuto adzatiyesa;

  Tingapezeke tikunyozedwa.

  Kulalikira kungavute,

  Tidzakhulupirirabe M’lungu.

  (KOLASI)

  Lalikira

  Indetu onse amve!

  Lalika,

  Dzikoli lisanathe.

  Lalika,

  Ofatsa amvetsetse.

  Lalika

  M’dziko lonse!

 3. 3. Nthawi zina tidzapeza,

  Anthu ofunadi kumvetsera.

  Tiwaphunzitsa ’pulumuke

  Dzina la Yehova tiyeretse.

  (KOLASI)

  Lalikira

  Indetu onse amve!

  Lalika,

  Dzikoli lisanathe.

  Lalika,

  Ofatsa amvetsetse.

  Lalika

  M’dziko lonse!