Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 NYIMBO 51

Tadzipereka kwa Mulungu

Sankhani Zoti Mumvetsere
Tadzipereka kwa Mulungu
ONANI

(Mateyu 16:24)

 1. 1. M’lungu wathu watikokera kwa Khristu

  Kuti azititsogolera.

  Cho’nadi tachidziwa,

  M’lungu watiphunzitsa.

  Ndipotu tadzikana,

  Tipita patsogolo.

  (KOLASI)

  Ifetu tadzipereka kwa Mulungu.

  Ndipo tikusangalala zedi.

 2. 2. Tamulonjezatu Yehova m’pemphero

  Kuti tidzamutumikira.

  Tilidi ndi chimwemwe,

  Timauzanso ena,

  Za dzina la Yehova,

  Ndi Ufumu wakenso.

  (KOLASI)

  Ifetu tadzipereka kwa Mulungu.

  Ndipo tikusangalala zedi.