Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 NYIMBO 103

Abusa Ndi Mphatso za Amuna

Abusa Ndi Mphatso za Amuna

(Aefeso 4:8)

 1. 1. Yehova amatithandiza,

  Kudzera mwa ’busa.

  Mwa chitsanzo chawo chabwino,

  Amatiphunzitsa.

  (KOLASI)

  M’lungu watipatsa amuna,

  Omwe timadalira.

  Amadera nkhawa tonsefe;

  Ndiyetu tiwakonde.

 2. 2. Abusawa ndi achikondi;

  Amaleza mtima.

  Tikapunthwa amathandiza,

  Kutitu tichire.

  (KOLASI)

  M’lungu watipatsa amuna,

  Omwe timadalira.

  Amadera nkhawa tonsefe;

  Ndiyetu tiwakonde.

 3. 3. Amatipatsa malangizo,

  Tisasocheretu.

  Tizisangalatsa Mulungu,

  Ndi kum’tumikira.

  (KOLASI)

  M’lungu watipatsa amuna,

  Omwe timadalira.

  Amadera nkhawa tonsefe;

  Ndiyetu tiwakonde.