Phunzirani kwa Anzake a Yehova—Zochita

Gwiritsani ntchito zochitazi kuti mupangenso zinthu zosiyanasiyana za m’mavidiyo a Phunzirani kwa Anzake a Yehova, ndipo kambiranani ndi ana anu mfundo zomwe mwaphunzira.

Abigayeli

Kodi mungaphunzire chiyani kwa Abigayeli yemwe anali mnzake wa Yehova?

Debora

Kodi mungaphunzire chiyani kwa Debora yemwe anali mnzake wa Yehova?

Pepani, palibe mawu ofanana ndi omwe mwasankha.